Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ndi a nyumba yonse ya Israyeli anasewera pamaso pa Yehova, ndi zoyimbira za mitundu mitundu za mlombwa, ndi azeze, ndi zisakasa ndi malingaka, ndi masece, ndi nsanje.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:5 nkhani