Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 6:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagawira anthu onse, ndiwo unyinji wonse wa Israyeli, amuna ndi akazi, kwa munthu yense mtanda wa mkate ndi nthuli ya nyama, ndi ncinci ya mphesa, Ndipo anthu aja onse anabwera yense ku nyumba yace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:19 nkhani