Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anadzitengera akazi ang'ono ena ndi akazi a ulemu ena a ku Yerusalemu, atafikako kucokera ku Hebroni; ndipo anambadwira Davide ana amuna ndi akazi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 5

Onani 2 Samueli 5:13 nkhani