Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rekabu ndi Baana ana a Rimoni wa ku Beeroti, anamuka, nafika ku nyumba ya Isiboseti potentha dzuwa popumula iye usana.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:5 nkhani