Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu anaturuka kwa Davide, natumizira Abineri mithenga, amene anambweza ku citsime ca Sira. Koma Davide sanacidziwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:26 nkhani