Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwamuna waceyo anapita naye, nanka nalira, namtsata kufikira ku Baburimu. Pomwepo Abineri ananena naye, Coka, bwerera; ndipo anabwerera.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:16 nkhani