Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mtima wa Davide unamtsutsa, atatha kuwerenga anthuwoo Davide nati kwa Yehova, Ndinacimwa kwakukuru ndi cinthu cimene ndinacita; koma tsopano Yehova mucotse mphulupulu ya mnyamata wanu, pakuti ndinacita kopusa ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:10 nkhani