Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 23:35-39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

35. Hezra wa ku Karimeli, Paarai M-aribi;

36. Igali mwana wa Natani wa ku Zoba, Bani Mgadi;

37. Zeleki M-amoni, Naharai Mbeeroti, onyamula zida za Yoabu mwana wa Zeruya;

38. Ira M-itri, Garebi M-itri;

39. Uriya Mhiti; onse pamodzi anali makumi atatu mphambu asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23