Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 23:30-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Benaya Mpiratoni, Hidai wa ku timitsinje ta Gaasi;

31. Abialiboni M-aribati, Azmaveti Mbahurimi;

32. Eliaba Mshaliboni wa ana a Jaseni, Jonatani;

33. Sama Mharari, Ahiamu mwana wa Sarari Mharari;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23