Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

niwapereka m'manja a Agibeoni, iwo nawapacika m'phiri pamaso pa Yehova, ndipo anagwa pamodzi onse asanu ndi awiri; m'masiku a kukolola, m'masiku oyamba, poyamba kuceka barele.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:9 nkhani