Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Agibeoni ananena naye, Sitifuna siliva kapena golidi wa Sauli kapena nyumba yace; ndiponso sitifuna kupha munthu ali yense wa m'Israyeli. Nati iye, Monga inu mudzanena, momwemo ndidzakucitirani.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:4 nkhani