Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 21:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Abisai mwana wa Zeruya anamthandiza namkantha Mfliistiyo, namupha. Pomwepo anthu a Davide anamlumbirira iye nati, Inu simudzaturuka nafenso kunkhondo, kuti mungazime nyali ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:17 nkhani