Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afilisti anaponyananso nkhondo ndi Aisrayeli; ndipo Davide anatsika ndi anyamata ace pamodzi naye naponyana ndi Afilisti; nafuna kukomoka Davide.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:15 nkhani