Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 20:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. ndi Adoramu anayang'anira msonkho; ndi Jehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri;

25. ndi Seva anali mlembi; ndi Zadoki ndi Abyatara anali ansembe;

26. ndiponso Ira Mjairi anali nduna ya Davide.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20