Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 20:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza nammangira misasa m'Abeli wa Betimaaka, naundira nthumbira pa mudziwo, ndipo unagunda tioga; ndipo anthu onse akukhala ndi Yoabu anakumba lingalo kuti aligwetse.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:15 nkhani