Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse a Yuda anayankha anthu a Israyeli. Cifukwa mfumu iri ya cibale cathu; tsono mulikukwiyiranji pa mrandu umenewu? tinadya konse za mfumu kodi? kapena kodi anatipatsa mtulo uli wonse?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:42 nkhani