Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti nyumba yonse ya atate wanga inali anthu oyenera imfa pamaso pa mbuye wanga mfumu; koma inu munaika mnyamata wanu pakati pa iwo akudya pa gome lanu. Kuyenera kwanga nkutaninso kuti ndikaonjeze kudandaulira kwa mfumu?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:28 nkhani