Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mefiboseti mwana wa Sauli anatsika kukakomana ndi mfumu; ndipo sadasamba mapazi ace, kapena kumeta ndebvu zace, kapena kutsuka zobvalazace kuyambira tsiku lomuka mfumukufikira tsiku lobwera kwao mumtendere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:24 nkhani