Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mnyamata wanu ndidziwa kuti ndinacimwa; cifukwa cace, onani, ndinadza lero, ndine woyamba wa nyumba yonse ya Yosefe kutsika kuti ndikomane ndi mbuye wanga mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:20 nkhani