Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco mfumu inabwera nifika ku Yordano. Ndipo Ayuda anadza ku Giligala, kuti akakomane ndi mfumu, ndi kumuolotsa mfumu pa Yordano.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:15 nkhani