Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisalomu amene tinamdzoza mfumu yathu anafa kunkhondo. Cifukwa cace tsono mulekeranji kunena mau akuti abwere nayo mfumuyo?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:10 nkhani