Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anauza Yoabu, Onani mfumu irikulira misozi, nilira Abisalomu.

2. Ndipo cipulumutso ca tsiku lila cinasandulika maliro kwa anthu onse; pakuti anthu anamva kuti, Mfumu iri ndi cisoni cifukwa ca mwana wace.

3. Ndipo tsiku lija anthu analowa m'mudzi kacetecete, monga azemba anthu akucita manyazi pakuthawa nkhondo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19