Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anthuwo anati, Simudzaturuka ndinu; pakuti tikathawa sadzatisamalira ife; ngakhale limodzi la magawo awiri a ife likafa sadzatisamalira; koma inu mulingana ndi zikwi khumi a ife; cifukwa cace tsono nkwabwino kuti mutithandize kuturuka m'mudzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:3 nkhani