Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahimaazi mwana wa Zadoki ananena kaciwiri kwa Yoabu, Komatu, mundilole ndithamange inenso kutsata Mkusi. Ndipo Yoabu anati, Udzathamangiranji, mwana wanga, popeza sudzalandira mphotho ya pa mauwo?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:22 nkhani