Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakufika Husai kwa Abisalomu, Abisalomuyo ananena naye, Ahitofeli analankhula mau akuti; ticite kodi monga mwa kunena kwace? ngati iai, unene ndiwe.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:6 nkhani