Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 16:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahitofeli ananena ndi Abisalomu, Mulowe kwa akazi ang'ono a atate wanu amene iye anawasiya kuti asunge nyumbayo; ndipo Aisrayeli onse adzamva kuti atate wanu aipidwa nanu; pomwepo manja a onse akukhala nanu adzalimba.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:21 nkhani