Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mnyamata wanu ndinawinda pakukhala ine ku Gesuri m'Aramu, ndi kuti, Yehova akadzandibwezeranso ndithu ku Yerusalemu, ine ndidzatumikira Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:8 nkhani