Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abisalomu anacitira zotero Aisrayeli onse akudza kwa mfumu kuti aweruze mrandu wao; comweco Abisalomu anakopa mitima ya anthu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:6 nkhani