Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo mfumu inanena kwa Itai Mgiti, Bwanji ulikupita nafe iwenso? Ubwerere nukhale ndi mfumu; pakuti uli mlendo ndi wopitikitsidwa; bwerera ku malo a iwe wekha.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:19 nkhani