Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata a mfumu ananena kwa mfumu, Onani, monga mwa zonse mbuye wathu mfumu adzasankha, anyamata anu ndife.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:15 nkhani