Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisalomu anaitana Ahitofeli Mgiloni, mphungu wa Davide, ku mudzi wace ndiwo Gilo, pamene iye analikupereka nsembe. Ndipo ciwembuco cinali colimba; pakuti anthu anacurukacurukabe kwa Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:12 nkhani