Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi wa ku Tekowayo ananena ndi mfumu, Mbuye wanga mfumu, mphulupulu ikhale pa ine ndi pa nyumba ya atate wanga; ndipo mfumu ndi mpando wacifumu wao zikhale zopanda cifukwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:9 nkhani