Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 14:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abisalomu nayankha Yoabu, Ona, ndinatumiza kwa iwe kuti, Bwera kuno kuti ndikutume kwa mfumu kukanena, Ine ndinabwereranji kucokera ku Gesuri? mwenzi nditakhala komweko; cifukwa cace tsono mundilole kuona nkhope ya mfumu; ndipo ngati mulinso mphulupulu mwa ine andiphe ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:32 nkhani