Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali akali panjira, mau anafika kwa Davide, kuti, Abisalomu anapha ana amuna onse a mfumu, osatsalapo ndi mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:30 nkhani