Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisalomu anakamulira anyamata ace, nati, Inu mukhale maso, mtima wa Amnoni ukasekera ndi vinyo, ndipo ine ndikati kwa inu, Kanthani Amnoni; pamenepo mumuphe, musaope; sindine ndakulamulirani inu mulimbike, citani camuna.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:28 nkhani