Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inati kwa Abisalomu, lai mwana wanga, tisapite tonse, kuti tingakucurukire. Ndipo iye anaiumirira koma inakana kupita; koma inamdalitsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:25 nkhani