Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisalomu sanalankhula ndi Arononi cabwino kapena coipa, pakuti Abisalomu anamuda Amnoni, popeza adacepetsa mlongo wace Tamara.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:22 nkhani