Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 12:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Davide ananyamuka pansi, nasamba, nadzola, nasintha zobvala; nafika ku nyumba ya Yehova, napembedza; pamenepo anafika ku nyumba yace; ndipo powauza anamuikira cakudya, nadya iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:20 nkhani