Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lacisanu ndi ciwiri mwanayo anamwalira. Ndipo anyamata a Davide anaopa kumuuza kuti mwanayo wafa, pakuti iwo anati, Onani, mwanayo akali moyo, tinalankhula naye, osamvera mau athu; tsono tidzamuuza bwang kuti mwana wafa; sadzadzicitira coipa nanga?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:18 nkhani