Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 9:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zikho zomwera zonse za Solomo zinali zagolidi, ndi zipangizo zonse za nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano zinali za golidi woona; siliva sanayesedwa kanthu m'masiku a Solomo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 9

Onani 2 Mbiri 9:20 nkhani