Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mpando wacifumuwo unali nao makwerero asanu ndi limodzi, ndi copondapo mapazi cagolidi, omangika ku mpandowo; ndi ku mbali zonse ziwiri za pokhalirapo kunali manja; ndi mikango iwiri inaimirira m'mbali mwa manjawo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 9

Onani 2 Mbiri 9:18 nkhani