Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

osawerenga uja anabwera naye amalonda oyendayenda, ndi amalonda ena; ndipo mafumu onse a Arabiya, ndi akazembe a dziko, anadza naye golidi ndi siliva kwa Solomo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 9

Onani 2 Mbiri 9:14 nkhani