Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo anampatsa mfumu yaikazi ya ku Seba cifuniro cace conse, ciri conse anacipempha, osawerengera zija adabwera nazo kwa mfumu. Momwemo anabwerera, namuka ku dziko lace, iyeyu ndi anyamata ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 9

Onani 2 Mbiri 9:12 nkhani