Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unacita bwino kuti unatero mumtima mwako;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:8 nkhani