Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mumvere Inu m'Mwamba, nimukhululukire chimo la akapolo anu, ndi la anthu anu Israyeli, mutawalangiza njira, yokoma ayenera kuyendamo, nimutumizire mvula dziko lanu limene munapatsa anthu anu likhale colowa cao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:27 nkhani