Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mumvere m'Mwamba, nimucite ndi kuweruzira akapolo anu, kumtsutsa woipayo, ndi kumbwezera chimo lace, ndi kulungamitsa wolungamayo, kumbwezera monga mwa cilungamo cace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:23 nkhani