Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Yehova Mulungu wa Israyeli, msungireni mtumiki wanu Davide cija mudamlonjezaco, ndi kuti, Sadzakusowa munthu pamaso panga wakukhala pa mpando wacifumu wa Israyeli; pokhapo ngati ana ako asamalira njira yao, kuti ayende m'cilamulo canga, monga umo unayendera iwe pamaso panga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:16 nkhani