Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe anaturuka m'malo opatulika, pakuti ansembe onse anali komwe adadzipatula, osasunga magawidwe ao;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 5

Onani 2 Mbiri 5:11 nkhani