Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapanganso magome khumi, nawaika m'Kacisi, asanu ku dzanja lamanja, ndi asanu ku dzanja lamanzere. Napanga mbale zowazira zana limodzi zagolidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4

Onani 2 Mbiri 4:8 nkhani