Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 36:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Iye anawakweretsera mfumu ya Akasidi, ndiye anawaphera anyamata ao ndi lupanga, m'nyumba ya malo ao opatulika, osacitira cifundo mnyamata kapena namwali, mkulu kapena nkhalamba; Mulungu anawapereka onse m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36

Onani 2 Mbiri 36:17 nkhani